Mzuni yatsekedwa kutsatira zionetsero za dzulo

Kutsatira zionetsero zomwe ophunzira aku Mzuzu University anachita dzulo lachisanu, akuluakulu a sukuluyi alamula ophunzira onse kuti achoke pasukuluyi mam’mawa wa lero loweruka. Malingana ndi kalata yomwe akuluakulu a sukuluyi atulutsa, ophunzira sakuloledwa kupezeka pa sukuluyi padakali pano. Ophunzirawa anachita zionetsero dzulo lachisanu ati pofuna kuti sukulu fees itsike. Mwazina iwo anayatsa moto komanso kutchinga […]

The post Mzuni yatsekedwa kutsatira zionetsero za dzulo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください