Mzuni itsekulira pa 19 m’malo mwapa 12 February

Sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu yalengeza kuti ophunzira omwe akupitiliza maphunzilo pasukuluyi adzayamba maphunzilo awo amchigawo choyamba lolemba pa 19 February 2024 m’malo mwa pa 12 February. Kudzera mchikalata chomwe Malawi24 yaona, sukuluyi ikudziwitsa anthu onse kuphatikizapo makolo ndi omwe amayang’anira ophuzilawa kuti yayika pa 19 February ngati tsiku loyambira maphunzilo kuchoka pa 12 February. […]

The post Mzuni itsekulira pa 19 m’malo mwapa 12 February appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください