Zina ukamva kamba anga mwala: Ku Kasungu anthu ena akuti afukula manda a m’bale wawo yemwe akuti anamwalira mosadziwika bwino zaka zinayi (4) zapitazo, ndipo anthuwo akukayikira ngati mafupa omwe awapeza alidi a munthu. Malingana ndi zomwe tsamba lino lapeza, nkhaniyi yachitika sabata ino m’mudzi wa Ng’ombe ku Chamama mdera la mfumu yayikulu Kapelula m’boma […]
The post Mwikho! Afukula manda am’bale wawo patatha zaka zinayi appeared first on Malawi 24.