Chipani cha Democratic Progressive (DPP) chati ndichodandaula ndi zomwe achita anthu ena omwe ang’amba komaso kuwotcha nsalu za chipani chawo ati kamba konyasidwa ndikuchotsedwa kwa a Kondwani Nankhumwa nchipanichi. Lamulungu lapitali, anthu ena omwe ena mwa iwo anavala zovala za makaka a DPP, anatchingira nsewu a Nankhumwa pomwe amachokera ku mwambo wa mapemphero ku Ndirande […]
The post Mwatilakwira — DPP yadandaula powotcheledwa nsalu appeared first on Malawi 24.