Bungwe lomenyera ufulu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) layamikira mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera poyankhula zomwe akuti zikusonyeza kumva kulira kwa a Malawi, ndipo HRDC yati uwu ndi utsogoleri omwe a Malawi amawufuna. Potsatira kuchepa mphamvu kwa ndalama ya Kwacha sabata yatha, lachitatu madzulo a Chakwera anayankhula ku mtundu wa Malawi ndipo […]
The post Mwamva kulira kwa a Malawi bwana – HRDC yayamikira Chakwera appeared first on Malawi 24.