Mwafwa tafwa! ankhonya athu awiri agwebedwa ku Tanzania

Inde chakachi achilowa nawo komatu achilowa nkhope zawo zitatupa fufufuu ngati mandazi. Wilson Masamba komanso Limbani Lano omwe kwathu kuno timawati anamatetule azigogodo, awona chidameta nkhanga mpala ku Tanzania komwe agwebedwa ngati mawa kulibe mpaka m’modziyo anachita kuthawa mu ling’i kuwopa kuphedwa ndi dzibonyongo. Masamba komaso Lano omwe mu chiyankhulo chaku masewero othidzimulanawa amatchulidwa kuti […]

The post Mwafwa tafwa! ankhonya athu awiri agwebedwa ku Tanzania appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください