Mvula yomwe inadza ya Mphamvu ndi mphepo yawononga sukulu ya pulayimale ya Mkhaza ku Linthipe 1 m’boma la Dedza. Malingana ndi m’modzi mwa aphunzitsi yemwe walankhula ndi Malawi24 a Josen Chaima ati Mvulayi inayamba dzulo lachitatu Masana koma inabwera ndi mphepo yamphamvu zomwe zinapangitsa kalasi limodzi kusasuka Malata. A Chaima ati ngoziyi sinavulaze aliyense pa […]
The post Mvula ya mphepo yawononga sukulu ku Dedza appeared first on Malawi 24.