Muwuzeni zowona mtsogoleri wathu – Chadza

M’modzi mwa anthu omwe amayankhulapo pazochitika m’dziko muno Lyford Chadza wapempha alangizi a mtsogoleri wa dziko lino kuti adzimuwunikira mtsogoleriyu mwatchutchutchu ponena kuti a Chakwera achedwa kulengeza kuti m’dziko muno muli njala. A Chadza ati zomwe anena  a Lazarus Chakwera pa uthenga wawo dzulo zimayenera kunenedwa kalekale pamene thumba la chimanga lidakwera mpaka nkumagulidwa pa […]

The post Muwuzeni zowona mtsogoleri wathu – Chadza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください