Mutharika wati MCP ikukoza zodzabera chisankho

Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ati chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chikukonza zoti chidzabele chisankho chosakha mtsogoleri wa dziko cha chaka cha mawa.  A Mutharika amayankhula izi Lamulungu pa Njamba munzinda wa Blantyre pomwe chipani chawo cha Democratic Progressive Party (DPP) chinachititsa nsonkhano wa ndale.  Poyankhula ku khwimbi la anthu lomwe […]

The post Mutharika wati MCP ikukoza zodzabera chisankho appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください