Mtsogoleri wa chipani cha DPP a Peter Mutharika atsindika okha koyamba kuti dziko la Malawi lilibe utsogoleri ndipo iwo akubwelanso kuzapulumutsa a Malawi kuchiwonongeko. “I, Peter Mutharika, am ready to lead DPP to victory again in 2025,” he says. Iwo atinso pali anthu ena omwe akufuna kubweretsa lamulo loti iwo asadzayimile kamba ka zaka zawo. […]
The post Mutharika wasindika kuti akubweleranso kudzapulumutsa a Malawi ku chionongeko appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.