Kuli kanthu kokanthula nchala mchipani cha Democratic Progressive (DPP) pomwe mtsogoleri wake a Peter Mutharika achotsa a Kondwani Nankhumwa pa udindo wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi mchigawo chakum’mwera. Izi ndimalinga ndi kalata yomwe chipani cha DPP yatulutsa lamulungu pa 10 December, 20 yomwe wasainira ndi mtsogoleri wa chipanichi a Mutharika. Malingana ndi chikalatachi, a […]
The post Mutharika wachotsa Nankhumwa pa udindo appeared first on Malawi 24.