Mtsogoleri opuma wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progress Party (DPP) Professor Arthur Peter Mutharika akufuna kuyankhula ndi mtundu wa a Malawi komanso mtsogoleri wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress Party (MCP) a Lazarus Chakwera. Malingana ndi mneneri wa a Mutharika, Shadrick Namalomba, mtsogoleriyu ayankhula lachitatu […]
The post Mutharika ayankhula ku mtundu wa a Malawi lachitatu appeared first on Malawi 24.