Nduna yowona za chuma a Simplex Chithyola Banda yati anthu ku Malawi kuno asamazinyenge kuti Kwacha inali ndi mphamvu isanagwetsedwe posachedwapa popeza ndalamayi ilibe mphamvu olo pang’ono. A Chithyola amayankhula izi lero ku BICC ku Lilongwe pa msonkhano wa atolankhani. “Takhala tikudzinyenga pomaonetsa ngati ndalama yathu ya Kwacha inali ya mphamvu koma kumeneko kunali kudzinyenga […]
The post Musazinyenge, Kwacha ilibe mphamvu olo pang’ono – nduna ya zachuma appeared first on Malawi 24.