‘Musayiponde fadah’ mutapapira mkalabongo komanso mankhwala ozunguza bongo

Apolisi ku Kasungu apempha anthu oyendetsa galimoto kuti ‘ ‘asayiponde fadah’ komanso asayendetse atapapira bibida komanso mankhwala ozunguza bongo pofuna kuti aliyense alowe mchaka chatsopano cha 2024  ndi moyo. Yemwe ndi komishonala wa apolisi mchigawo chapakati ku  m’mawa a Rhoda Manjolo ndi omwe ayankhula izi kumadyelero omwe amachitikira pa sukulu ya sekondale ya Loyola m’bomali. […]

The post ‘Musayiponde fadah’ mutapapira mkalabongo komanso mankhwala ozunguza bongo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください