Musawamvele achule omwe akukuletsani kuyenda – a Matola awuza Chakwera

Nduna yoona zamphavu yamagetsi a Ibrahim Matola awuza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti asamvele achule omwe akufuna kuti a Chakwera asiye kuyendayenda, ndipo a Matola ati dziko lino likuyenda bwino. A Matola amayankhula izi Lolemba pa 6 June ku Golomoti m’boma la Dedza komwe mtsogoleri wa dziko linoyu amakhazikitsa ntchito yapanga mphamvu […]

The post Musawamvele achule omwe akukuletsani kuyenda – a Matola awuza Chakwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です