Musalowetse ndale – wachenjeza Bushiri

Mtsogoleri wa mpingo wa ECG – Jesus Nation, Shepherd Bushiri, wachenjeza anthu omwe akulowetsa ndale pa ntchito yake yogawa chimanga kwa anthu omwe akhudzidwa ndi njala kuti asiye ponena kuti iye akupanga izi kungofuna kuthandiza. Bushiri wayankhula izi Loweluka pa 17 February, 2024 pomwe anali m’boma la Thyolo komwe amapitiliza ntchito yogawa chimanga yomwe wayikhazikitsa […]

The post Musalowetse ndale – wachenjeza Bushiri appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください