Nthambi yowona za pamsewu ya Directorate of Road Traffic and Safety Services (DRTSS) yaletsa anthu kuti asamapiteso kuma ofesi awo ndi ziphuphu ponena kuti nthambiyi ndiyosinthika tsopano. Izi ndi malingana ndi chithunzi cha chikwangwani chomwe chikuoneka kuti chaikidwa kuma ofesi a nthambi ya DRTSS chomwe pano anthu akugawana m’masamba a mchezo. Pachithuzichi palembedwa mawu oletsa […]
The post Musadzabwerenso ndi ziphuphu kuno, yatero nthambi ya DRTSS appeared first on Malawi24.