Mulandu wa malemu Wittika: Khoti likumanaso lachiwiri mulungu wa mawa

Oweruza milandu Mzonde Mvula wayamba wayimitsa kaye kumva mlandu wa a Lester Maganga omwe akuwaganizira kuti anapha a Allan Witika mpakana pa 9 April chaka chino. Izi zili chomwechi chifukwa choti mboni ziwiri zaboma zomwe zimayenera kupelekera umboni sizinabwere. Bwaloli limayembekezeka kupitiliza kumva mlanduwu kuyambira lero kufikira lachinayi sabata ino. A Mvula atinso adzadziwitsa pa […]

The post Mulandu wa malemu Wittika: Khoti likumanaso lachiwiri mulungu wa mawa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください