Mukati a Giddes asamaimbe ku “show”, muziwadyetsa? – wang’alura Pemphero Mphande

M’modzi mwa anthu otchuka pa fesibuku, Pemphero Mphande wauza anthu onse omwe akunena kuti mzilazembe pa maimbidwe a Giddes Chalamanda akula asamakaimbe ku ma “show”, kuti ayambe kupeleka ndalama zothandizira umoyo wa tsiku ndi tsiku wa chiyambakaleyu. Chatsitsa dzaye kuti njobvu ithyoke nyanga nchakuti, lero lachisanu kuyambira 6 koloko madzulo, a Chalamanda akuyenera kukaimba kuphwando […]

The post Mukati a Giddes asamaimbe ku “show”, muziwadyetsa? – wang’alura Pemphero Mphande appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください