Mukang’amba ticket, kungani ina. Osaonetsa mtima onyanyala – Chakwera

Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wati a Malawi ochuluka akudzinyonga kamba ka mtima wa chifooko. Polankhula ku Mzuzu pamene anapita kukapemphera, a Chakwera ati a Malawi sakuchedwa kufooka mu nyengo zowawa zomwe akudutsa. “Anthu ambiri akuzipha chifukwa chotaya chikhulipiliro msanga,” anatero a Chakwera. Iwo anati anthu aphunzire kulimbikitsana wina ndi mzake kuti asataye […]

The post Mukang’amba ticket, kungani ina. Osaonetsa mtima onyanyala – Chakwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください