Mayi Easter Gondwe omwe akasumilidwa kuti akhala akunyoza nthiti ya oyimba Zeze Kingston, Dorothy, pa fesibuku, ayima pachulu ndikuuza onse omwe akuwavera chisoni kuti adzililire okha ngakhale zikuveka kuti munthu wina wa chiwiri wakawamang’aliraso. Izi zikudza pomwe Dorothy yemweso amadziwika ndi dzina loti ‘Cash Madam’, wakamang’ala ku bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe kuti Gondwe […]
The post Mudzililire nokha, bweretsani samanizo – wabweza moto Easter Gondwe appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
