Mtsogoleri aliyese amanunkha fungo loipa losava pelefyumu, watero Nkasa

…wati anthu akudzipha chifukwa alibe chiyembekezo …wati otsutsa boma anali odzikonda muulamuliro wawo Atatenga nthawi asanatulutse nyimbo yatsopano, chiyamba kale pamaimbidwe, Joseph ‘Phungu’ Nkasa, wadandaulira munthu amene akuti anatsitsira mpweya dziko lino ponena kuti mtsogoleri aliyese amene dziko lino lakhala naye amanunkha fungo la minyamalo. Nyimbo yatsopanoyi yomwe mutu wake ndi ‘Tithawire kwa Iye’, yatulutsidwa […]

The post Mtsogoleri aliyese amanunkha fungo loipa losava pelefyumu, watero Nkasa appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください