Mtsikana wadziphera m’nyumba ya bwenzi lake

Mtsikana wa zaka 17 wadzipha podzimangilira ndi neti yozitetezera ku udzudzu m’nyumba ya chibwezi chake pomwe amachokera ku sukulu ya sekondale ya Mphande m’boma la Mwanza. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Mwanza Sergeant Hope Kasakula, mtsikanayu yemwe wazindikilidwa ngati Kithuwe Mtunduwatha wapanga izi sabata yatha pa 25 October, 2023 m’mudzi mwa Mchotseni, m’dera […]

The post Mtsikana wadziphera m’nyumba ya bwenzi lake appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください