Mtolankhani wakale wa Matawi24 wamangidwa polemba nkhani yokhudza oganizilidwa katangale Batatawala

Apolisi mu mzinda wa Blantyre amanga yemwe anali mtolankhani wakale wa Malawi24 McMillan Mhone, kamba kolemba nkhani yokhudza munthu woganiziridwa katangale a Abdul Karim Batatawala chaka chatha. Pa 15 August chaka chatha, Malawi24 idatulutsa nkhani yomwe imakamba zambiri zokhudza momwe a Batatawala akuganizilidwira kuti anaphwanya malamulo kuti apeze ma kontalakiti ndi boma la Malawi. M’nkhaniyo, […]

The post Mtolankhani wakale wa Matawi24 wamangidwa polemba nkhani yokhudza oganizilidwa katangale Batatawala appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください