Mtengo was shuga wafika K2600: A Malawi adandaula ati athawire kuti?

A Malawi ambiri akulira mokweza kamba kakupitilira kwa kukwera mtengo wa zinthu monga packet la shuga lomwe madera ambiri likugulisidwa pakati pa K2400 ndi K2600. Nyasatimes inayankhula ndi anthu osiyana siyana kuchokera m’mbali zosiyana mdziko muno ndipo ambiri akuwonesa kugonja ndi kuthodwa chifukwa katundu akukwerabe mtengo komanso katunduyo amapangidwa konkuno. Koma mkulu wa kampani yopanga […]

The post Mtengo was shuga wafika K2600: A Malawi adandaula ati athawire kuti? appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください