Mtengo wa shuga wapitilira K3500

Pomwe kusowa kwa shuga kwafika pa mwana wakana phala m’dziko muno. Ogulitsa malonda omwe akumapezeka ndi katunduyu sakutchaja mosekelera ndipo m’madera ena shugayu watsala pang’ono kufika pa mtengo wa K4000 pa paketi imodzi. Lachinayi pa 7 March, 2024, Malawi24 inayendera ina mwa misika komaso masitolo akuluakulu munzinda wa Blantyre omwe ndikuphatikizapo Sana Cash & Carry […]

The post Mtengo wa shuga wapitilira K3500 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください