Pomwe mtsogoleri wa dziko lino analongedza kale zovala kuti anyamuke lero lachitatu kupita m’dziko la Saudi Arabia ndi anthu osachepera 70, msonkhano omwe amayenera kupitira wa Africa-Arab Summit walepheleka. Lachiwiri sabata ino boma linalengeza kuti a Chakwera anyamuka Lachitatu kupita m’dziko la Saudi Arabia komwe akakhale nawo pa mkumano wa mayiko a mu Africa komaso […]
The post Msonkhano ku Saudi Arabia walepheleka, Chakwera apitabe? appeared first on Malawi 24.