Mpira wa miyendo wa atsikana ukuyenda bwino – Migogo

Mtsogoleri wa  bungwe la National Women’s Football a  Adelaide Migogo wati mphoto imodzi  yomwe Malawi yapeza yomwe wawina Leticia Chinyamula kukhala osewela yemwe adzakhale wapamwamba mtsogolomu zawonetsa kuti osewerawa ali ndi kuthekera kochita bwino kwambiri mtsogolomu akamalowa nawo mu mipikisano yambiri. Poyankhula  ndi wayilesi ina m’dziko muno a  Migogo apempha boma kuti lithandize mpira wa […]

The post Mpira wa miyendo wa atsikana ukuyenda bwino – Migogo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください