Mphunzitsi wanjatidwa kamba kobela anthu ponena kuti ndi wapolisi

A polisi mu mzinda wa Lilongwe ku Area 3, anjata  a Jonathan Nkhosa yemwe ndi mphunzitsi wa kupulayimale wa zaka 51 zakubadwa, kamba kobera anthu powanamiza kuti ndi wapolisi. A Nkhosa akhala akuchita bodza kwa abale a anthu omwe ali mkusungidwa mchitokosi cha apolisi powauza kuti alipire ndalama kuti m’bale wawo atuluke pa belo. Yemwe […]

The post Mphunzitsi wanjatidwa kamba kobela anthu ponena kuti ndi wapolisi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください