Mphunzitsi wa Flames ndi opanda nzeru, watero Gwamba

Katswiri oyimba nyimbo za chamba cha hip-hop Gwamba wanena kuti mphunzitsi wa timu ya dziko lino Marian Mario Marinica ndiopanda nzeru kamba kosapereka mpata okwanira kwa Peter Banda. Mukulankhula kwake kudzela pa samba la mchezo la Facebook, Gwamba wanena kuti mphunzitsi oganiza mwanzeru sangalephere kupereka mpata kwa mnyamata waluso ngati Peter Banda. “Pano tikambe zampira. […]

The post Mphunzitsi wa Flames ndi opanda nzeru, watero Gwamba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です