Mphunzitsi amupeza osalakwa pa mlandu ogwililira mwana

Bwalo la milandu mu mzinda wa Zomba lapeza Chisomo Francisco Gomani, yemwe ndi mphunzitsi pa sukulu ya pulaimale, wosalakwa pa mlandu womuganizila kuti anagwililira  mwana wachichepere. Gomani adamangidwa ndi polisi ya Chingale pa 27 October 2023 pomuganizila kuti adagonana ndi mwana yemwe anali wophunzira pa sukulu yomwe iyeyu amaphunzitsapo. Atamangidwa, wachibale wake Temweka Chirwa, anapita […]

The post Mphunzitsi amupeza osalakwa pa mlandu ogwililira mwana appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください