Mphunzitsi ali mchitokosi kamba kogwililira mwana

Apolisi m’boma la Rumphi akusunga mchitokosi wachiwiri kwa mphunzitsi wamkulu pa sukulu ya Mzungutwa a Wonderson Shaba a zaka 34 zakubadwa powaganizira kuti anagwililira mtsikana wa zaka 14. Mneneri wa apolisi m’boma la Rumphi, Noel Kamchenga ndiye watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti bambo Shaba anapalamula mlanduwu kuchokera mwezi wa November, 2023 mpaka February, 2024. “Mayi […]

The post Mphunzitsi ali mchitokosi kamba kogwililira mwana appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください