Ophunzira okwana 17 ochokera pa sukulu ya pulayimale ya Chawe m’boma la Chiradzulu, ali manja m’khosi pomwe zadziwika kuti salemba nawo mayeso a sitandade 8 kamba koti mphunzitsi wina pa sukuluyi anawadyera ndalama yolipilira mayesowa omwe akulembedwa sabata ino. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Chiradzulu a Cosmas Kagulo omwe azindikira m’phunzitsiyu […]
The post M’phunzitsi adya ndalama za ophunzira 17 za mayeso a sitandade 8 appeared first on Malawi 24.