Ophunzira 30 pa sukulu ya sekondare ya Seven Hills pa Chimbiya ku Dedza salemba nawo mayeso a MANEB a Form 2 ndi Form 4 kaamba koti mphunzitsi wa mkulu pasukuluyi anawadyera ndalama zawo za mayeso . Ena mwa ophunzirawa auza Zodiak kuti ndizokhumudwitsa kuti mtsogoleri wawo yemwe wawachita chipongwe. Mwini wake wa sukukuyi a […]
The post Mphunzitsi adya ndalama za mayeso za ophunzira 30, akanika kulemba mayeso appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.