Mtsikana wazaka 20 yemwe anamangidwa mu 2021 kamba kakupha “mwangozi” mwana wake wa chaka chimodzi ndi miyezi 9, lero ali ndi chimwemwe chodzadza tsaya pomwe wamasulidwa ndipo wauzidwa kuti asapalamuleso mlandu uli onse kwa chaka chimodzi. Mtsikanayu yemwe dzina lake ndi Mphatso Kaonga ochokera ku Nthalire m’boma la Chitipa, anamangidwa ali ndi zaka 18 pomuganizira […]
The post Mphatso: Khothi lamasula mtsikana opha mwana wake appeared first on Malawi 24.