Mpaseni dimba Chisaleyo: a Malawi ayamikira Kazembe wa Amerika

Anthu mdziko muno makamaka pamasamba a mchezo ayamikira komaso kudabwitsika ndi zintchito za kazembe wa dziko la Amerika a David Young omwe sabata ino anathandiza mayi wina kuphika mandasi ndipo analawanso mandasiwo. A Young omwe anabwera mdziko muno mwezi wa March chaka chino, anatutumutsa anthu pomwe anayendera a Margaret Makhuza omwe amaphika mandasi ku Area […]

The post Mpaseni dimba Chisaleyo: a Malawi ayamikira Kazembe wa Amerika appeared first on Malawi 24.

close

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

Generated by Feedzy