Chinantindi cha anthu chikupitiriza kutsata ndi kukonda Jetu ngakhale kuti makosana a Podcast Malawi anapereka ganizo lakuti gogoyu asiye kuyimba chifukwa alibe luso pamayimbidwe. Patangopita masiku ochepa chabe a Podcast Malawi chiyakhulireni zokhwatcha Jetu, gogoyu wakatekesa ku sukulu yaukachenjede ya MUBAS mzinda wa Blantyre. Ophunzira pa sukuluyi sanawerengere mkomwe zomwe Podcast Malawi inayankhula ndipo anamunyadira […]
The post Moto wa Jetu ukana kuzilala, apata puloti appeared first on Malawi 24.