Mnyamata wa zaka 18 wamangidwa chifukwa chogwirilira mwana wa zaka zitatu

Wyson Salad wa zaka 18 amumanga ku Balaka pomuganizila kuti anagwirilira mwana wa zaka zitatu. Mneneri wa polisi ya Balaka a Gladson M’bumpha ati izi zinachitika pa 1 September, 2023 ndipo oganizilidwayo, yemwe ndi amalume ake a mwanayo, wamangidwa dzulo. A M’bumpha ati pa 1 September nthawi ya kumasana a Salad omwe amachita bizinesi ya […]

The post Mnyamata wa zaka 18 wamangidwa chifukwa chogwirilira mwana wa zaka zitatu appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください