Mnyamata wa zaka 16 wagwililira gogo wa Zaka 74

Apolisi m’boma la Ntchisi akusunga mchitokosi mnyamata wa zaka 16 atagwililira  gogo wa zaka 74. Malingana ndi Mneneli wa apolisi  ku chigawo cha pakati kum’mawa a Esther Mkwanda, nthawi ya kumasana pa tsikuli  mnyamata anatsatila  kumunda komwe gogoyu amakasaka nkhuni ndipo anamumanga manja ndi kukolopola zovala za gogoyu mkumuchita za kusalungamazo. Apolisi ati gogoyu anakafotokozera […]

The post Mnyamata wa zaka 16 wagwililira gogo wa Zaka 74 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください