Mnyamata wa Form 2 ku Likangala Secondary School akufuna thandizo

Humphry Likaka, mnyamata yemwe akuphunzira ku Likangala Secondary School ku Zomba ndipo ali mu Form 2, ali pa chiopsezo chosiya sukulu chifukwa chosowa thandizo. Humphry yemwe ndi ovutikitsitsa amakhala ndi malume ake kwa Kazembe omwe ndiwovutika ndipo amachitita kupemphetsa (masikini) mu mzinda wa Zomba kuti apeze chokudya. Iye wauza Malawi24 kuti moyo wafika povuta popeza […]

The post Mnyamata wa Form 2 ku Likangala Secondary School akufuna thandizo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください