Bwalo lamilandu ku Mangochi lapeza olakwa m’neneri Christopher Phiri wa mpingo wa Supernatural Embassy pa mlandu oseweretsa malo obisika a mwana wawo wa mkazi zomwe akuti zinali ndi kuthekera koti anakagonana naye. Apolisi kumapeto kwa mwezi watha, anamanga mneneri Phiri omwe ndi azaka powaganizira kuti amagonana ndi mwana wawo wa mkazi wa zaka 16 koma […]
The post Mneneri Phiri wapezeka olakwa pa mlandu ochita za akuluakulu ndi mwana wake appeared first on Malawi 24.