Bwalo la Midima Senior Resident Magistrate mumzinda wa Blantyre latulutsa pa belo mzika ya m’dziko la India a Ramsigng Narissing Shinde azaka 57 omwe akuganiziridwa kuti anagwililira mwana wazaka 5. A Shinde anamangidwa pa 13 June chaka chino ndi apolisi aku Limbe powaganizira kuti anagwililira mwana wa zaka zisanu ku Maone komwe amakhala moyandikana ndi […]
The post M’mwenye oganizilidwa kugwililira mwana wa zaka 5 watuluka pa belo appeared first on Malawi24.