Nzika ya dziko lino a Eddie Longwe omwe amakhala m’dziko la Kuwait ati ali ndi chidwi chopikisana nawo pa zisankho za mtsogoleri wadziko lino zomwe zikuyembekezeka kuchitika chaka chamawa. A Longwe auza Malawi24 kuti iwo ndiwokonzeka kuombola amalawi omwe pakadali pano akukumana ndimavuto osiyanasiyana mu ulamuliro wa presidenti Lazarus Chakwera. Iwo ati ali ndinfundo zikuluzikulu […]
The post M’malawi okhala ku Kuwait akufuna kupikisana nawo pa mpando wa mtsogoleri wadziko lino appeared first on Malawi 24.