Apolisi m’dziko la South Africa amanga nzika ya dziko la Malawi ndi anthu ena atatu akunja powaganizira kuti anaba ma galimoto awiri a mtundu wa Toyota Fortuner ndi Mercedes Benz zomwenso amafuna azizembetse kutuluka nazo m’dzikolo. Malingana ndi ofalitsa nkhani za a Polisi ya m’boma la Limpopo, Brigadier Hlulani Mashaba, anthu atatuwa amangidwa kumathelo a […]
The post M’malawi ndi ena atatu akunja amangidwa ku South Africa appeared first on Malawi 24.