Patapita nthawi ma bizinezi ambiri atasokonekera mmbali mwa Nyanja ya Malawi kamba kakusefukila kwa madzi, a National Water Resources Authority (NWRA) ati tsopano mlingo wa madzi mu mnyanjayi ukuphwera. Malingana ndi mneneri wa bungweli, a Masozi Kasambala izi zikudza kamba koti mvula yomwe imagwa ku Tanzania komanso mchigawo cha ku mpoto kwa dziko lino ikutsika. […]
The post Mlingo wa madzi mnyanja ya Malawi ukutsika appeared first on Malawi 24.