Mlendo ndimame sachedwa kukamuka: Mneneli Mbewe watuluka PP

Pomwe anthu otsatira chipani cha People’s (PP) anali ndi chimwemwe chodzadza tsaya kuti mwina mkutheka Mneneli David Mbewe awatengera mtsidya lina, munthu wa Mulunguyu watuluka mchipanichi atakhalamo maola ochepa. Mneneli Mbewe analowa chipani cha PP lachinayi pa 11 August ndipo mwambo omulandira mkuluyu unachitikira mu mzinda wa Lilongwe komwe akuluakulu achipani cha PP anati ndiosangalala […]

The post Mlendo ndimame sachedwa kukamuka: Mneneli Mbewe watuluka PP appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください