Oweluza Milandu ku bwalo lalikulu a Mzondi Mvula apeleka chitsogozo chakuti mulandu wa a Lester Maganga ukhala ndi masiku khumi ndi anayi (14) kuti umvedwe ndipo kuti oganizilidwawa akakhalebe akusungidwa m’manja mwa a chitetezo kufikila mtsogolo.. Mu kumvedwa kwa mulanduwu lero ku bwalo lalikulu mu mzinda Lilongwe a Lester Maganga akana kuti iwo si olakwa […]
The post Mlandu wa Lester Maganga ulowanso mu bwalo mwezi wamawa appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
