Woyimba Mlaka Maliro akuti Malawi wasochera pa ulendo wake waku Canaan kotero sitikafika kamba koti ndodo yotisogolera yasowa. A Maliro awuza atolankhani izizi atawafunsa kuti anenepo pa nyimbo yomwe ayimba koma sinatulusidwe kaye. Mu nyimbo iyi, yotchedwa ndodo, a Maliro akuti: Yasowa, yasowa, yasowa mama ndodoya Moses. Ulendoopitaku Canaan, wavuta tikupita ku Libya. Mama yasowa! […]
The post Mlaka Maliro ang’alura Chakwera mu nyimbo: Ati ulendo wa ku Canaan sitikafika appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.
Moni Malawi 
