Mkumano wa makhansala ku Zomba walephereka chifukwa chachisokonezo

Mkumano wa nambala 19 wama Khansala komanso wa Phungu yekhayo wamu mzinda wa Zomba omwe pachingerezi umatchedwa Full Council walephereka chifukwa chachisokonedzo chomwe chidabuka munyumbayi. Makhansala achipani cha DPP komanso Phungu wachipani cha DPP Bester Awali adafunsa Mfumu ya Mzinda wa Zomba Khansala Davie Maunde kuti ndichifikwa chiyani adalepheretsa mkumano womwe umayenera kuchitika Lachisanu pa […]

The post Mkumano wa makhansala ku Zomba walephereka chifukwa chachisokonezo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください