Mkulu amene analonjeza zokhululukila okuba nkhuku atha kukakhala ku ndende

Ukayenda siya phazi, mulomo umatsata. Mawu awa atha kukhala ndi amene akulingalira a Saulos Chilima pamene atoledwa ndi a polisi poganizilidwa kuti anachita za katangale ndi a Zunneth Sattar. Bungwe lothetsa ziphuphu la ACB, lamanga wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima kamba kokhudzidwa ndi nkhani za katangale. Malinga ndi chikalata chimene atulutsa […]

The post Mkulu amene analonjeza zokhululukila okuba nkhuku atha kukakhala ku ndende appeared first on Malawi 24.

close

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

Generated by Feedzy